Ogwira ntchito anayi apa kampani yogulitsa zipangizo za ulimi ya Export Trading Group (ETG) awanjata ndikuwaponya mchitokosi cha apolisi ku Dowa kamba kowaganizira kuti adakwangwanula m’matumba afetereza pa kampanipo. Anthu anayi oganizilidwawa ndi a Sigele Selemani azaka 25, a Tionge Mazibuko azaka 37, a Gabriel Kayange azaka 31 komanso Fabiano Banda azaka 26 zakubadwa. Nkhani […]
The post Ogwira ntchito anayi pa kampani ya ETG awanjata kamba kogwinya feteleza appeared first on Malawi 24.