Ogwililira mwana wake omupeza agamulidwa kukakhala ku ndende zaka zisanu ndi chimodzi

Bwalo lozenga milandu ku Balaka lagamula bambo wa zaka 23 zakubadwa, a Thomas Kanyimbo, kugagwira ntchito ya kalavulagaga  ku ndende kwa zaka zisanu ndi chimodzi (6) kaamba kopezeka olakwa pa mlandu ogwililira mwana wake omupeza wa zaka zisanu ndi ziwiri (7). Oimira boma pa milandu, Sub Inspector Liston Sabola, adauza bwalo la milandu kuti bamboyu […]

The post Ogwililira mwana wake omupeza agamulidwa kukakhala ku ndende zaka zisanu ndi chimodzi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください