Mfumu Chawola ya dera la Kangoi yomwe ili pansi pa Mfumu ya yikulu Timbiri M’boma la Nkhata Bay yati iyo limodzi ndi anthu awo ndiwokondwa kuti tsopano ntchito za umoyo pa chipatala chaching’ono cha Kangoi ziyamba kuyenda bwino. Mfumuyi yanena izi pomwe Bambo Lloyd Ndhlozi omwe akufuna kuzapikisana pa mpando wa ukhansala ku wadi ya […]
The post Ofuna kuyimira pa mpando wa khansala wamanga nyumba ya mlangizi ku Nkhata Bay appeared first on Malawi 24.