Amene anali ndi chiyembekezo choti awona kugawana zida pakati pa chipani cha UTM ndi zipani zina mu mgwirizano wa Tonse ayembekeze kaye pang’ono kaamba koti a Saulos Chilima ati akufuna kumwera nsuzi ndipo sangasambe mmanja nsima isanathe. A Chilima anayankhula izi lachisanu ku nyumba yawo ku Lilongwe komwe anapeleka malonje kwa khwimbi la anthu lomwe […]
The post Ofuna kumwera nsuzi sasamba m’manja nsima isanathe – Chilima appeared first on Malawi 24.