Ofesi ya zaumoyo ku Zomba yayamba kupereka mankhwala a Likodzo

Ofesi yadza Umoyo Boma la Zomba yati yayamba kupereka mankhwala alikodzo komanso mankhwala a njoka zammimba kwa ana omwe ndi oyambira zaka zisanu (5) zakubwadwa kulekedza zaka khumi ndi zisanu zakubwadwa (15). Wofalitsa nkhani ku ofesi yadza Umoyo Boma la Zomba Arnold Mndalira ndiyemwe wayankhula idzi Lolemba pansonkhano wa atolankhani. Mndalira wati ofesiyi ikuyembekedzereka kulandiritsa […]

The post Ofesi ya zaumoyo ku Zomba yayamba kupereka mankhwala a Likodzo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください