Ofesi ya zaumoyo ikufufuza za imfa ya anthu asanu ku Blantyre

Ofesi ya Zaumoyo m’boma la Blantyre yati ikufufuza za imfa ya anthu asanu omwe amwalira kutsatira atamwa mowa osadziwika bwino ndipo ofesiyi yati idzabweretsa poyera zotsatira zakafukufuku-yi akatha. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe khonsolo ya mzinda wa Blantyre yatulutsa ndipo wasayinira ndi mkulu wa za umoyo a Dr. Gift Kawalazira. Kudzera mkalatayi ofesiyi yati […]

The post Ofesi ya zaumoyo ikufufuza za imfa ya anthu asanu ku Blantyre appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください