Yemwe amayankhulapo pankhani zosiyanasiya zochitika m’dziko muno a Francis Liyati, adzuzura akulu akulu a zamaphunziro m’boma la Mzimba posalabadira ndi kuthana ndi nkhani za nkhanza zomwe m’phunzitsi wa mkulu pa sukulu ya Mzimba LEA Joseph Chirwa akuchitira aphunzitsi achizimai. Chidzudzulochi chikudza pomwe pali nkhani yakuti m’phunzitsi wa mkuluyu akumawachitira nkhanza aphunzitsi akazi powakakamiza kuti akhale […]
The post Ofesi ya za maphunziro m’boma la Mzimba ayidzudzula appeared first on Malawi 24.