Odwala khate adandaula za kusalidwa

A Thomas Damiyano a m’mudzi mwa Kazembe Mfumu yaikulu Kachindamoto M’boma la Dedza ati chiwapezereni ndi nthenda ya Khate chaka chatha moyo wawo sunasinthe kwenikweni chifukwa akukwanitsabe kugwira ntchito zomwe zimawapezetsa ndalama pa moyo wawo wa tsiku ndi tsiku koma adandaula kuti amasalidwa ndi anzawo ena. Makolo ake a Thomas komanso abale ake awiri nawonso […]

The post Odwala khate adandaula za kusalidwa appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください