Ochita malonda mumsika waukulu wa Zomba sakukondwa ndikukwera kwa chiphaso

Anthu ochita malonda mumsika waukulu wa Zomba ati sakukondwera ndizomwe achita akulu akulu akhonsolo ya mzindawu pokweza mtengo wachiphaso kuchoka pa K200 kufika pa K300 patsiku. Wapampando wa anthu ochita malondawa a Ayatu Chidothe ati Khonsolo ya mzinda wa Zomba yafulumira kukwedza mtengo wodulira chiphasochi popeza masiku ano zinthu sizikuyenda ndipo ochita malonda sakuchita phindu […]

The post Ochita malonda mumsika waukulu wa Zomba sakukondwa ndikukwera kwa chiphaso appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください