Anthu ena omwe akudzitchula kuti nzika zokhudzidwa ati achita m’bindikilo kuma ofesi onse a nthambi yowona zolowa ndi zotuluka ya DICS pofuna kukakamiza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti achotse ntchito mkulu wa nthambiyi komaso nduna yokhudzidwa. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe nzika za nchigawo chakum’mwera zalembera khonsolo ya mnzinda wa Blantyre […]
The post Nzika zokhudzidwa zichita m’bindikilo ku maofesi onse a Immigration appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
