Mzika ina ya m’dziko la Niger yomwe anaimbwandila lachiwiri pa bwalo la ndege la Kamuzu mu mzinda wa Lilongwe ipitilira kuyankha mulandu wake opezeka ndi makhwala owopsya ku malo ochitila chimbudzi mawa atayikaniza belo. Mzikayi yomwe dzina lake ndi Osman Mohamed wa zaka 30 ayikaniza belo itakaonekela ku bwalo la milandu la Mkukula ku Lumbadzi […]
The post Nzika ya ku Niger ayikaniza Belo appeared first on Malawi 24.