Apolisi ku Limbe mu mzinda wa Blantyre amanga nzika ina ya dziko la China kaamba kovulaza mayi yemwe anadandaula kuti anamugulitsa belo la zovala zong’ambika. Izi ndimalingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Limbe a Patrick Mussa omwe azindikira nzika yaku China yi ngati a Jiqo Chi Ping omwe ndimwini wake wa shopu ya Yibo […]
The post Nzika ya ku China yakhapa kasitomala ku Blantyre appeared first on Malawi 24.