Nyumba ya boma yachotsa wothilira maluwa pomuganizira kuti amaulura zinsinsi

Mayi yemwe amagwira ntchito yosamala maluwa a Tiyanjane Mlangeni, omwe akuganizilidwa kuti ndiosasunga pakamwa ndipo akhala akuwulura zinsinsi zochuluka zokhudza kumpanda, inde ku nyumba ya boma, achotsedwa ntchito. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe boma latulutsa yomwe wasainira ndi Shadreck L Ching’oma m’malo mwa mlembi wankulu wa boma a Colleen Zamba yomwe ikusonyeza kuti a […]

The post Nyumba ya boma yachotsa wothilira maluwa pomuganizira kuti amaulura zinsinsi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください