Pofika lero pa 27 December 2023, nyimbo ya Atoht Manje yomwe mutu wake ndi ‘Nchape’ tsopano yaoneledwa ka 1.1 miliyoni pa YouTube mu miyezi iwiri yokha. Iyi ndi nyimbo ya Atoht yomwe yaoneledwa kwambiri pa nyimbo zomwe oyimbayu anaika pa tsamba lake la pa Youtube. Nchape inalinso nyimbo yomaliza yomwe Atoht anatulutsa asanamwalire. Katswiriyu adamwalira […]
The post Nyimbo ya malemu Atoht Manje ‘Nchape’ yaoneledwa ka 1.1 miliyoni pa YouTube appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 