Kudamveka kufuula mwa chisangalalo pamene azimai adaimba nthungululu komanso malikhweru adamveka pakati pa abambo ndi achinyamata pamene kampani ya Escom imakonza vuto la magetsi lomwe lidali ku Majiga 2 ntauni ya Balaka. Anthu okhala mdelari akhala opanda magetsi kwa mwezi wathunthu malingana ndi kuonongeka kwa makina a Transformer omwe adapsa. Izi akuti zidakhudza kwambiri anthuwa […]
The post Nthungululu komanso malikhweru ku Balaka: Escom yakonza vuto la magetsi appeared first on Malawi 24.