Nthawi ya DPP katangale analipo koma sanafike apapa — Ben Phiri

Phungu wadera lapakati m’boma la Thyolo a Ben Phiri, adzudzula boma la Tonse kaamba kosaonetsa chidwi pofuna kuthetsa katangale mdziko muno ndipo ati mu ulamuliro wa DPP katangale analipo koma ati sanafike mlingo omwe wafika pano. A Phiri omwe amayankhula izi kwa atolankhani lachinayi mumzinda wa Lilongwe pakutha pazokambirana za nyumba ya malamulo zomwe zili […]

The post Nthawi ya DPP katangale analipo koma sanafike apapa — Ben Phiri appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください