Nthambi ya za nyengo yikuti mchigawo chakumwera ndi pakati anthu ayembekezere mvula yambiri kuyambira lero

Nthambi yoona za nyengo ndi kusintha kwa nyengo yati madera a mchigawo chakumwera komanso pakati pa dziko lino ayembekezere mvula ya mphamvu komanso ya mabingu kuyambira m’mawa uno kufikila Lachisanu likudzali. Mvulayi ati ikhala ya mphamvu kaamba ka dera lozetsa mvura lotchedwa ITCZ. Izi ndi malingana ndi ulosi wamomwe nyengo ikhalire kuyambira lero mpaka pa […]

The post Nthambi ya za nyengo yikuti mchigawo chakumwera ndi pakati anthu ayembekezere mvula yambiri kuyambira lero appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください