Nthambi yowona za Nyengo ndi kusintha kwa Nyengo mdziko muno yalosera nyengo la dzinja mchaka chino ndi cha mawa (2024/2025) kuti kukhala mvula yochuluka poyelekeza ndi dzinja lapitali. Mkulu woyang’anira nthambiyi, a Lucy Mtilatila awuza atolankhani mu mzinda wa Lilongwe la chisanu kuti ngakhale zili chomwechi, Pali chiyembekezo chakuti mwezi wa November utha kukhala ndi […]
The post Nthambi ya za Nyengo alosera mvula yochuluka mnyengo ya mchaka chino ndi cha mawa appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.