Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera wakhazikitsa ntchito yomanga zipinda zophunzilira 10,900 komanso malo osinthira 1000 pansi pa ntchito ya MARP. Polankhula pa mwambowu omwe ukuchitikira pa sukulu ya purayimare ya Chikololere Ku Dedza, Dr. Chakwera ati iyi ndi njira yoonetsetsa kuti ana akuphunzilira malo abwino msukulu za dziko lino. Malinga ndi mtsogoleriyu ntchitoyi […]
The post Ntchito yomanga zipinda zophunzirira 10 900 za pulayimale yayambika appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.