Boma ndithandizo lochokera ku Global Fund likukumba mijigo mmadera osiyanasiyana a mmdziko muno pofuna kuchepetsa matenda omwe amabwera kamba ka madzi. Polankhula pomwe anayendera imodzi mwa ntchito yomwe ikuchitika ku Biya m’boma la Nkhata bay, wachiwiri kwa nduna ya zaumoyo Mayi Halima Daud anati ndi cholinga cha boma kufuna kuti anthu a mdziko muno akhale […]
The post Ntchito yokumba mjigo m’boma la Nkhata Bay yayambika appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.