NRB yatsimikizira aMalawi kuti ikugwira ntchito yake mwa ukadaulo

Bungwe loyendetsa kalembera m’dziko muno la National Registration Bureau (NRB) lati ilo likupitilira kugwira ntchito yake mwaukadaulo ngakhale pali madandaulo kuchokera kwa mzika zina zokhudzidwa kuti kalemberayi sakuyenda bwino. Izi zadza pamene gulu la mzika zokhudzidwa zati pali andale ena omwe akumauza ana omwe sanakwane zaka 16 kuti akalembetse mukaundula ndicholinga choti adzavote mu chisankho […]

The post NRB yatsimikizira aMalawi kuti ikugwira ntchito yake mwa ukadaulo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください