Chakula chinkulirano pakati pa oyimba wa makono ndi wina wamvula zakale, ndipo zili ngati dzana likumenyana ndi mawa pomwe JB akuponyerana zibonyongo ndi K Banton; mwanayo akadzati unakwatira nkhalamba, wankuluyo koma chiphuzo cha kuno ndi ukoo. Awawa aleletseni apwetekana. Oyimba Khumbo Storrah otchedwa K Banton ndi oyimba nzake Alberto Fernando Zacharias otchedwa Jolly Bro mwachidule […]
The post Nkhondo ya Angitawo: JB diso kwa diso ndi KB appeared first on Malawi 24.