Nkhalamba ayi pa Mpando wa President – a Welani Chilenga akubweretsa bilu yothana ndi Mutharika

Nkhondo ya pa chiweniweni ya ku chipani chotsutsa cha DPP ikupitilira, tsopano akufuna kulikhirana ku malamulo a dziko. A Welani Chilenga amene anathotholedwa mu chipani limodzi ndi a Nankhumwa ati nkhalamba zisamayimire nawo pa zisankho. Malinga ndi chikalata chimene Malawi24 yaona, a Chilenga ati iwo akufuna kusintha malamulo a dziko lino. Mu chikalatachi chimene chikupita […]

The post Nkhalamba ayi pa Mpando wa President – a Welani Chilenga akubweretsa bilu yothana ndi Mutharika appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください