Adindo awapempha kuti achite machawi kuthetsa nkangano omwe wafika posauzana m’mudzi mwa mfumu Limera m’boma la Machinga komwe anthu sakumwerana madzi, ndipo akumamenyana pali ponse pomwe angakumanepo kamba ka malo olima mpunga omwe akulimbirana. Tsamba lino lapeza kuti anthu a m’mudzi mwa mfumu Limera akulimbirana malo ena olima mpunga omwe ali kufupi ndi nyanja ya […]
The post Nkangano wa malo olima mpunga wavuta ku Machinga appeared first on Malawi 24.