Njovu yapha mayi ku Dedza

Njobvu imodzi mwa ziwiri zomwe zinatuluka m’nkhalango ina m’boma la Dedza, yapha mayi wa zaka 45. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Dedza, Beatrice Jefita, yemwe wazindikira malemuwo ngati a Volontina Yonasi omwe akuti akumana ndi tsokali Lachiwiri pa 16 April, 2024. A Jefita awuza nyumba zina zoulutsa mawu mdziko muno kuti […]

The post Njovu yapha mayi ku Dedza appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください