Njonda ina yafa pomwe imafuna kuba Nsomba

Njonda ina yazaka 30 zakubadwa m’boma la Mangochi yatsikira kulichete itamira panthawi yomwe iyo imafuna kuba nsomba mumisampha ya asodzi amzake pa doko lina mnyanja ya Malombe. Nkhani yonse ikuti mkuluyu yemwe dzina lake ndi Issaah Kamwendo, lolemba pa 26 February adazemba pakati pa usiku watsikulo ndikupita padokolo ndikuyamba kuba nsombazo mumatchera anzake. Apa mwadzidzi […]

The post Njonda ina yafa pomwe imafuna kuba Nsomba appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください