Mfumu Kapelura ya m’boma la Kasungu yati imodzi mwa njobvu zomwe zinatuluka mu nkhalango ya Nkhotakota yavulaza munthu mdera lawo. Malingana ndi mfumuyi, njobvu zisanu ndi ziwiri ndi zomwe zinatuluka ku nkhalango yotetezekayi ndi kulowa m’mudzi mwawo lachinayi. Iwo anati anthu anachita chidwi ndi njobvuzi ndipo anayamba kuzilondola pamene ena amazigenda ktui zibwelere ku nkhalango. […]
The post Njobvu yavulaza munthu ku Kasungu appeared first on Malawi 24.