Nthambi yoona za nyengo yati madera ambiri m’dziko muno maka mu chigawo cha kum’mwera ndi pakati, ng’amba ikhala ikupitilira kwa sabata imodzi kamba koti mphepo ya mvula ikuombera dziko la Tanzania. Ngakhale izi chili chomwechi, mkulu wa nthambiyi, Dr Lucy Mtilatila ati anthu asadere nkhawa kamba koti mphepo ya mvulayi ikhala ikubwereraso m’dziko muno posachedwa. Mu […]
The post Ng’amba ikhala ikupitilira sabata – atero a zanyengo appeared first on Malawi 24.