Mtsogoleri wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers Thom Mpinganjira wachenjeza ochemelera timuyi makamaka aku Lilongwe pa nkhani yoyambitsa ziwawa, ndipo wati masewero aliwose aziyitanitsa apolisi okhala ndi mfuti kuti akathane ndi maliwongo aliyese. Izi ndi malingana ndi kanema wina yemwe anthu akugawana pa masamba a nchezo yemwe akuwonetsa mpondamatikuyu akuyankhula za timu yawo ya Wanderers […]
The post Ndizipanga hayala apolisi a mfuti – Mpinganjira wachenjeza ochemelera Wanderers appeared first on Malawi 24.