Inu nonse munadzadzana pa Njamba lamulungu, yang’anani kumbali. Ndipo inu mumayesa kuti 2025 ndi ya a Chilima, talikilani. Uthenga uli pano ndi wa onse okondwa ndi a Chakwera. Iwo ati 2025 ino akupitiriza, zotuluka m’boma muiwale. Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera lero auza mtundu wa a Malawi kuti iwo ayimanso chaka chamawa ndipo […]
The post “Ndiyimanso, ndipo ndiwinanso,” watero Chakwera appeared first on Malawi 24.