“Ndinyasi”: Sindikudzapikisana nawo pa chisankho cha 2025 — watero Bushiri

…ati iwo si asataniki …ati iwo sanayambane ndi Mlaka Mtsogoleri wa mpingo wa ECG Jesus Nation mneneri Shepherd Bushiri wanenetsa kuti iye siwandale ndipo wati sakudzapikisana nawo pa mpando wa utsogoleri wadziko pa chisankho cha mchaka cha 2025. Bushiri amayankhula izi pomwe amayankhula ndi wailesi ya Times momwe wafotokoza zinthu zambiri zomwe aMalawi akhala akufuna […]

The post “Ndinyasi”: Sindikudzapikisana nawo pa chisankho cha 2025 — watero Bushiri appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください