…wati anthu akuzuzika kwambiri pano kusiyana ndi nthawi ya DPP …wati sadzawakhululukira a Steven Kayuni Wachitetezo wamkulu wa mtsogoleri wakale wa dziko lino Peter Mutharika, a Norman Paulos Chisale sanafuna kusunga zakukhosi pomwe awulura kuti akuzunzika kaamba ka ndale ndipo ati onse omwe akuwazuza pano, ayembekeze kudzayankha kutsogoloku. A Chisale omwe pano ali ndi zaka […]
The post Ndine okwiya kwambiri, mudzayankha mukundipangazi – walira mokweza Norman Chisale appeared first on Malawi 24.