Ndinakadziwa sinkanapanga, tikhululukileni aMalawi – wanong’oneza bondo Mtambo, Kaliati

Pomwe ntchito yofuna kudzigulira malo m’mitima ya a Malawi yafika mlingo wina, Timothy Mtambo wati anakadziwa kuti zidzakhala chonchi, sanakapanga zionetsero zomwe zinathandiza m’gwirizano wa Tonse kutenga boma, ndipo naye Patricia Kaliati wapepesa a Malawi pa malonjezo osakwanilitsidwa. A Mtambo omwe ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha Alliance For Democracy (AFORD), ayankhula izi lamulungu […]

The post Ndinakadziwa sinkanapanga, tikhululukileni aMalawi – wanong’oneza bondo Mtambo, Kaliati appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください