Ndimadyera momwemo: Mr Jokes akana kugulilidwa mano

…wapempha kuti angomupatsa ndalamazo Katswiri pa nthabwala m’dziko muno Andrea Thonyiwa yemwe amadziwika kwambiri ndi dzina loti ‘Mr Jokes’, wakanitsitsa mwayi omwe anthu ena anamupatsa kuti apite m’dziko la South Africa kuti akamugulire mano. Malipoti pa masamba a mchezo akusonyeza kuti gulu la a Malawi ena omwe ali m’dziko la South Africa linachita nsonkhensonkhe kuti […]

The post Ndimadyera momwemo: Mr Jokes akana kugulilidwa mano appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください