Ndife wokonzeka kuchititsa zisankho – MEC

Bungwe lowona za zisankho la Malaŵi Electoral Commission (MEC) lanenetsa kuti kuyenda bwino kwa  zisankho zapatatu mu 2025 kudalira kuti anthu amvetse bwino ndondomeko ya kayendetsedwe kazisankhozi. M’modzi mwa makomishonala a bungweli, Dr Anthony Mukumbwa, anena izi lachinayi ku Mzimba pa msonkhano wolimbikitsa mafumu, atsogoleri a mipingo, mabungwe a Civil Society (CSOs) ndi ena onse […]

The post Ndife wokonzeka kuchititsa zisankho – MEC appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください