Patangodutsa maola ochepa woyimba wamkazi Tuno atadandaula za kusakondedwa, naye Temwa Gondwe wadandaula zomwezo ndipo akudzifusa kuti ‘Ndili kuti’ pomwe anthu ena awugogodi ayamba kumutoza Chatsitsa dzaye kuti njovu ithyoke nyanga nchakuti, mkati mwasabatayi, Temwah yemwe ndimwini wake wa nyimbo ya ‘Mvetsera’ yomwe anaimba limodzi ndi Zeze ndipo chaka chatha yawonongetsa anthu ndalama, anayika pa […]
The post Ndidalakwa chiyani, kepana ndisiye kuyimba? – wadandaula Temwa appeared first on Malawi 24.