Ndavomeleza koma ndikusinkhasinkha zochita – watelo Nankhumwa

Patangodutsa maola ochepa khothi la apilo ku Blantyre litakana pempho la a Kondwani Nankhumwa, Grezelder Jeffrey komaso Cecilia Chazama loti abwezeletsedwe mmaudindo awo ku chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP), a Nankhumwa ati achilandira chigamulochi koma akuti akusinkhasinkha ndi kufusafusa zoti achite momwe zatelemu. A Jeffrey, a Nankhumwa komanso mayi Chazama anakamang’ala ku bwalo […]

The post Ndavomeleza koma ndikusinkhasinkha zochita – watelo Nankhumwa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください