Ndathetsa mgwirizano ndine osati timu, samandilipira — watelo Khuda Myaba

…wati timu yomwe ingamufune ku Malawi ilimbe mthumba Mphangala yosewera mpira wa miyendo Khuda ‘Ikena’ Myaba wati iye ndamene wathetsa mgwirizano ndi timu ya Tishreen SC ya ku Syria kamba koti siyimamupatsa makobidi ndipo wati atha kusewera ku mpanje kuno ngati timu yomwe imufune ingakwanitse kumulipira. Myaba yemwe anapita ku timu ya Tishreen SC mwezi […]

The post Ndathetsa mgwirizano ndine osati timu, samandilipira — watelo Khuda Myaba appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください