“Ndani amapeza vuto ine ndikamwa mowa?” – wadabwa Namadingo

…wati u Doc wake pano ndiwa #DocAnavaya osati wa UNISA Ngati munalibe bandulo ya intaneti kumathero a sabata yatha, zambiri zakuphonyani, komabe tikutsinani khutu pang’ono: Oyimba Patience Namadingo watsindika kuti iye siwoyimba nyimbo zauzimu, mukamuona alithapsa musadabwe, bibida amachita naye akatelo amakwera Mercedes Benz yake ndipo pamwamba pa zonsezo, akuti vuto lalikulu m’dziko muno ndi […]

The post “Ndani amapeza vuto ine ndikamwa mowa?” – wadabwa Namadingo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください