Mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus McCarthy Chakwera wati ndi wokhumudwa ndi khalidwe la andale ena amene akulowetsa ndale pa nkhani ya njala yomwe yagwa mdziko muno. Polankhula m’mzinda wa Blantyre pomwe amatsegulira chipatala cha matenda a khansa cha International Blantyre Cancer Centre (IBCC), Chakwera wati akudziwa kuti andale ena adzimudzudzula iye ngati amene wabweretsa […]
The post Ndale zonyoza sizitereka nsima – Chakwera appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.