“Ndale zaku Malawi ndizaufiti”: Mtambo wati sanagwilitse munthu ntchito

…ati zionetsero zija ankafuna kusintha zinthu …ati boma lapitalo linkafuna kuwapha A Timothy Mtambo omwe posachedwapa anali nduna ya mgwirizano, atsutsa mwantu wa galu kuti anangowagwiritsa anthu ntchito pochita ziwonetsero kuti iwo apeze zomwe ankakhumbira. A Mtambo anena izi madzulo a lachiwiri pa 22 August pomwe amacheza ndi nyumba yofalitsa mawu ya Zodiak mu pologalamu […]

The post “Ndale zaku Malawi ndizaufiti”: Mtambo wati sanagwilitse munthu ntchito appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください