Ndalama ya gala ku MAGU yafika mpaka K250,000

…sukulu yati omwe sapanga nawo gala apelekebe ndalamayi Pomwe amaona ngati athana nazo zopeleka vindalama vitalivitali, ophunzira omwe amaliza maphunziro pa sukulu ya ukachenjede ya Malawi Assemblies of God University (MAGU), akuyeneraso kupisaso m’matumba ndikupeleka ndalama ya gala yomwe yafika mpaka K250,000. Sukulu ya ukachenjede ya MAGU yalengeza kuti mwambo otsazikana ndi ophunzira omwe amaliza […]

The post Ndalama ya gala ku MAGU yafika mpaka K250,000 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください