Ndachimina, watero panza Ichocho

Monga malemu John ‘Izeki’ Nyanga ananena kale kuti “zina umangoona waziyamba,” panza Yassin ‘Ichocho’ Suwedi wachimina ndipo akuziguguda pachifuwa uku akuyankhula yekha yekha kuti kodi moyowu unkalinda kuteleku? Panzayu apempha anduna kuti amukhululukile. Potsatira zomwe nduna ya zachitetezo a Ken Zikhale Ng’oma analamula kuti kampani ya Ichocho Power Security (IPS) ilandidwe chiphaso, mwini wake wa […]

The post Ndachimina, watero panza Ichocho appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください