Nankhumwa wati ndege ya ku Israel ikuzatenga achinyamata 221 ku Malawi

Mtsogoleri wa mbali yotsutsa mu Nyumba ya Malamulo, a Kondwani Nankhumwa, wati m’dziko muno mukuyembekezeka kufika ndege kuchokera m’dziko la Israel kuzatenga achinyamata 221 kuti akagwire ntchito mu dziko la Israel. Nankhumwa wapempha  unduna wa za ntchito kuti ufotokoze chilungamo chenicheni pa za ntchito yomwe achinyamata akukagwira mu dziko la  Israel. Malingana ndi a Nankhumwa, […]

The post Nankhumwa wati ndege ya ku Israel ikuzatenga achinyamata 221 ku Malawi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください