A Kondwani Nankhumwa, a Grezelder Jeffrey komanso a Cecilia Chazama ati sakumvetsetsa kuti bwalo la milandu ku Lilongwe linavomeleza kusinthidwa maudindo awo mu chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP) ndipo atatuwa akagwadwa ku bwalo lamilandu la apilo kuti abwezeretsedwe m’maudindo awo. Izi zikudza pomwe bwalo la milandu lalikulu ku Lilongwe kumapeto kwa mwezi wa […]
The post Nankhumwa, Jeffrey sakumvetsa, akamang’ala ku khothi la apilo appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 