M’modzi mwa akatswiri pandale mdziko muno wachenjeza a Kondwani Nankhumwa kuti akuyenera kupanga chiganizo mosamala pa zatsogolo lawo pandale ponena kuti akapanda kusamala atha kudzikumbira okha dzenje lomwe iwo sangathe kutulukamo. Malingana ndi Katswiriyu, a Lyford Chadza, a Nankhumwa akamapanga chiganizo chawo pazokhudza tsogolo lawo pandale asapusitsike kwambili ndi anthu omwe akuwachemerela kamba koti anthu […]
The post Nankhumwa atha kudzikumbira dzenje lomwe sangathe kutulukamo akapanda kusamala, watero katswiri pa ndale appeared first on Malawi 24.