Nankhumwa apempha boma liganizire omwe adasewerapo mpira wamiyendo ndi wa manja m’mbuyomu

Mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma m’nyumba ya malamulo a Kondwani Nankhumwa omwenso ndi phungu wa dera la Mulanje Central, apempha unduna woona za masewero kuti uganizire anthu omwe adasewerapo mpira wa miyendo komanso wa manja m’mbuyomu. A Nankhumwa ati n’zomvetsa chisoni kuona a namandwa ena omwe adasewerapo mpira bwino m’mbuyomu akuvutika kwambiri.   Mwachitsanzo a […]

The post Nankhumwa apempha boma liganizire omwe adasewerapo mpira wamiyendo ndi wa manja m’mbuyomu appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください