Namondwe wa Freddy: Phungu wa dera la Zomba Chingale wapempha thandizo

Phungu wa dera la Zomba Chingale Lonnie Phiri wati anthu a mu dera lake omwe akhudzidwa ndi Namondwe wa Freddy akusowa zinthu zosiyanasiyana zofunika pamoyo wao watsiku ndi tsiku. Phiri wauza Malawi24 kuti mdera la Zomba Chingale anthu pafupifupi 3,000 nyumba zawo zidagwa ndi mvula ya Namondwe ndipo akukhala m’malo anai (ma camp) komanso zinthu […]

The post Namondwe wa Freddy: Phungu wa dera la Zomba Chingale wapempha thandizo appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください