Nthambi Yoona Zanyengo ndi Kusintha kwa Nyengo m’dziko muno yati Namondwe wotchedwa Filipo wafika m’dziko la Mozambique ndipo akuti apangitsa kuti madera ena m’dziko muno alandire mvula ya mphamvu. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe nthambiyi yatulutsa lero Lachiwiri chomwe chikusonyeza kuti namondwe wa Filipo wafika m’dziko la Mozambique m’mawa wa lero pa 12 March, […]
The post Namondwe Filipo wafika ku Mozambique appeared first on Malawi 24.