“Mwayamba za ndale?” Anthu angoti kukamwa pululu pamene Dr Namadingo amene amadziwikanso bwino ndi dzina loti Doc walengeza kuti “2030 boma” ndipo anthu akhale tcheru. Izi zadzetsa mafunso ochuluka kwa anthu amene amamutsatira bwino. Namadingo wanena izi kudzera pa tsamba lake la mchezo la Facebook lero chakumadzulo ano, pamene iye wangolemba kuti “2030 Boma.” “Mwayamba […]
The post Namandingo wati 2030 boma appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 